Tuesday, June 18, 2013

CHILUNGAMO CHIDZIWIKE KWA A MALAWI


.
<Mukawelenga,gawilani anzanu nao awoneko>

  1. Boma la  ulamuliro wa PP  lidanamiza anyamata kuti apita Ku South Korea kukagwira ntchito
  2. Boma la  ulamuliro wa PP  silikuchitapo kanthu kuteteza Nyanja ya Malawi
  3. Boma la  ulamuliro wa PP  lidaoletsa chimanga Pamene a Malawi ankavutika ndi njala
  4. Boma la  ulamuliro wa PP  lidagwetsa ndalama komabe chuma chinapitilira  kusayenda bwino
  5.  Boma la  ulamuliro wa PP  limagawa mchenga mmalo mwa  feteleza kwa a Malawi
  6. Boma la  ulamuliro wa PP  ndilakatangale ndi ziphuphu zoospa kusiyana ndi DPP/UDF
  7. Boma la  ulamuliro wa PP  lidagula magalimoto amanyado a nduna Pamene zipatala zidalibe mankhwala
  8. Boma la  ulamuliro wa PP  likuononga ndalama ndi maulendo amudziko muno komanso kunja omwe phindu lake silikuoneka kwa a Malawi
  9. Boma la  ulamuliro wa PP  limaononga ndalama zambiri pama alawansi  kukagawa ufa wandalama zochepa kwambiri
  10. Boma la  ulamuliro wa PP  limanyoza komanso kutukwana a ndale otsutsa mmalo mokamba mfundo zotukula Malawi
  11. Boma la  ulamuliro wa PP  tidaona maliro akumadulidwa maliseche  ku motchale Pamene kuphana ndi umbanda udalinso  osasimbika.
  12. Boma la  ulamuliro wa PP  likugwiritsa ntchito nyumba zofalitsa uthenga za radio 1 ndi 2 komanso television ya Malawi molakwika
  13. Boma la  ulamuliro wa PP  likuononga ndalama zomwe zinakakhoza kugula mankhwala muzipatala ndi kubweza ndalama kwa anthu omwe ma kontalakiti awo adathetsedwa mosatsata malamulo
  14. Boma la  ulamuliro wa PP   lidagwilitsa ntchito ndalama mosasamala  mubajet  ya  chaka 2012/2013 ndindalama zopitilira ma billion
  15. Boma la  ulamuliro wa PP   limangomvera zilizonse zomwe azungu akuwauza ngakhale zili zosapindulira a Malawi
  16. Boma la  ulamuliro wa PP  limadana komanso  kumenya atolankhani kamba kolemba zinthu zosawakomera
  17. Boma la  ulamuliro wa PP  likumangotseka ma  masukulu ndimakoleji kamba kamavuto achuma komanso kudana ndi chilungamo anthu akamadandaula mmene zinthu ziliri mudziko lino
  18. Boma la  ulamuliro wa PP  likuononga ndalama pa milandu yomwe ilibe ntchito komanso yosapindulira a Malawi
  19. Boma la  ulamuliro wa PP  silikuganizila za umoyo wa anthu ogwira ntchito mmboma pankhani ya malipilo  komanso ma alawansi awo ngakhale umphawi wafika povuta kwa a Malawi ambiri.
  20. Boma la  ulamuliro wa PP  muzipatala mankhwala ofunikila komanso mafuta agalimoto za ambulansi akumasowa zomwe zikuthandizila kuluza miyoyo ya a Malawi omwe anali ndi udindo otukula dziko lathu lino

Zili ndi inu kupitilira kunamizidwa kuti zinthu zili bwino koma ngati muli okonda dziko lanu moganizenso mofatsa.

Gawilani anzanu kuti nao awonenso.


No comments:

Post a Comment